Thru the Bible Chichewa

TTB Chichewa

Pologalamu ya Tisanthule Baibulo ndi gawo limodzi lautumiki, ophunzitsa Baibulo, otchedwa ulendo m??baibulo (Thru the Bible). Mndandanda wamapogalamuwu unakonzedwa ndi Dr. J. Vernon McGee ndipo unatanthauzidwa mu zilankhulo zoposa zana zimodzi (100). Zinakonzedwa kuti pologalamu imodzi idzikhala ya mphindi makumi atatu (30) ndipo kuti pomaliza zidzathe kuthandiza omvera kumvetsetsa Baibulo lonse. Ndipo pakali pano mapologalamu onsewa tawaika pamakina a Intaneti. Ndife oyamika kuti mwasankha kuphunzira zambiri zokhudza mau a Mulungu kudzera mmapologalamuwa. Tikukulimbikitsani kuti mudzimvera po...

Não deixe de visitar o site do podcast e apoiar quem o produz: ttb.twr.org

Autor

Thru the Bible Chichewa

Categoria

Religion

Site do podcast

ttb.twr.org

Último episódio

30 de out de 2024

Onde ouvir?

Podcasts no app Replaio Radio Em breve

Os podcasts estão chegando ao app. Instale agora e seja o primeiro a descobrir um jeito totalmente novo de curtir podcasts

Baixe no Google Play Instale grátis Android 5 mi+ downloads · nota 4,8 iOS em breve

Episódios

Simeoni Ndi Anna Azindikira Mesiya; M’nyamata Yesu Ali M’kachisi; Kuyambika Kwa Utumiki Wa Yohane 20.12.2023
Zinthu Zomwe Zinachitika Kwa Mariya 19.12.2023
Nyimbo Za Khisimisi 18.12.2023
Kulengeza Kwa M’ngelo Gabrieli 15.12.2023
Chiyambi Ndi Kuonetsa Cholinga Cha Bukhuli 14.12.2023
Kugwiritsa Ntchito Pangano 13.12.2023
Tsogolo La Mtundu Wa Israyeli 12.12.2023
Chaka Chopuma Ndi Chaka Chachikondwerero 11.12.2023
Choyikapo Nyali Ndi Mkate Woonekera 08.12.2023
Kupitiliza Kuona Za Nyengo Yopatulika 07.12.2023
Nyengo Kapena Nthawi Yopatulika 06.12.2023
Kudetsedwa Kwa Unsembe Ndi Maliro 05.12.2023
Chilango Cha Kupha 04.12.2023
Ubale Wa Munthu 01.12.2023
Makhalidwe Oyenera Ya Ana Amulungu 30.11.2023
Pali Malo Amodzi Operekera Nsembe 29.11.2023
Tsiku Lotetezera 28.11.2023
Kuunika Zo Ukha 27.11.2023
Mabala Akukha Kapena Mabala Otuluka Magazi 24.11.2023
Mwambo Woyeretsa Munthu Wakhate 23.11.2023
Kupitiliza Kuona Nkhani Ya Khate 22.11.2023
Tikambirana Za Nthenda Ya Khate 21.11.2023
Kutengera Uchimo Kuchokera Kwa Makolo Kapena Kuti Kupatsirana Machimo Kuchokera Kwa Makolo 20.11.2023
Nyama Zodetsedwa Ndi Zosadetsedwa 17.11.2023
Chakudya Cha Anthu A Mulungu 16.11.2023

Ouça o podcast TTB Chichewa no Replaio

Rádio e podcasts em um só app - grátis e sem cadastro. Instale hoje e não perca o lançamento

Baixe no Google Play

O Replaio não é o publicador dos podcasts; os nomes dos programas, as capas e o áudio pertencem aos seus autores e são distribuídos por feeds RSS públicos