Thru the Bible Chichewa
TTB Chichewa
Pologalamu ya Tisanthule Baibulo ndi gawo limodzi lautumiki, ophunzitsa Baibulo, otchedwa ulendo m??baibulo (Thru the Bible). Mndandanda wamapogalamuwu unakonzedwa ndi Dr. J. Vernon McGee ndipo unatanthauzidwa mu zilankhulo zoposa zana zimodzi (100). Zinakonzedwa kuti pologalamu imodzi idzikhala ya mphindi makumi atatu (30) ndipo kuti pomaliza zidzathe kuthandiza omvera kumvetsetsa Baibulo lonse. Ndipo pakali pano mapologalamu onsewa tawaika pamakina a Intaneti. Ndife oyamika kuti mwasankha kuphunzira zambiri zokhudza mau a Mulungu kudzera mmapologalamuwa. Tikukulimbikitsani kuti mudzimvera po...
Koniecznie odwiedź stronę podcastu i wesprzyj twórcę: ttb.twr.org
Autor
Thru the Bible Chichewa
Kategoria
Strona podcastu
Ostatni odcinek
30 paź 2024
Gdzie słuchać?
Podcasty w aplikacji Replaio Radio Już wkrótcePodcasty trafią do aplikacji już wkrótce. Zainstaluj teraz i jako pierwszy zobacz nowe podejście do podcastów
Odcinki
Podobne podcasty
Replaio nie jest wydawcą podcastów; nazwy audycji, okładki i audio należą do ich autorów i są rozpowszechniane przez publiczne kanały RSS