Thru the Bible Chichewa

TTB Chichewa

Pologalamu ya Tisanthule Baibulo ndi gawo limodzi lautumiki, ophunzitsa Baibulo, otchedwa ulendo m??baibulo (Thru the Bible). Mndandanda wamapogalamuwu unakonzedwa ndi Dr. J. Vernon McGee ndipo unatanthauzidwa mu zilankhulo zoposa zana zimodzi (100). Zinakonzedwa kuti pologalamu imodzi idzikhala ya mphindi makumi atatu (30) ndipo kuti pomaliza zidzathe kuthandiza omvera kumvetsetsa Baibulo lonse. Ndipo pakali pano mapologalamu onsewa tawaika pamakina a Intaneti. Ndife oyamika kuti mwasankha kuphunzira zambiri zokhudza mau a Mulungu kudzera mmapologalamuwa. Tikukulimbikitsani kuti mudzimvera po...

Não deixe de visitar o site do podcast e apoiar quem o produz: ttb.twr.org

Autor

Thru the Bible Chichewa

Categoria

Religion

Site do podcast

ttb.twr.org

Último episódio

30 de out de 2024

Onde ouvir?

Podcasts no app Replaio Radio Em breve

Os podcasts estão chegando ao app. Instale agora e seja o primeiro a descobrir um jeito totalmente novo de curtir podcasts

Baixe no Google Play Instale grátis Android 5 mi+ downloads · nota 4,8 iOS em breve

Episódios

Chiyambi Cha Bukhu Ndi Kuwerengedwa Kwa Ana A Israyeli 24.01.2024
Yesu Adziwonetsa Kwa Anthu Ambiri Ndi Kukwera Kumwamba 23.01.2024
Yesu Ayikidwa M’manda Ndi Kuuka Kwa Akufa 22.01.2024
Yesu Achoka Kubwalo La Milandu Kupita Kukapachikidwa 19.01.2024
Amgwira Yesu Ndipo Apita Naye Kumabwalo Ya Mirandu 18.01.2024
Zochitika Zomwe Zikuonetsa Kumalizika Kwa Utumiki Wa Yesu 17.01.2024
Yesu Ayankha Funso Lakuti Kodi Zinthu Izi Zidzaoneka Liti? 16.01.2024
Yesu Akufunsidwa Za Ulamuliro Wake Ndipo Yesu Akuwayankha 15.01.2024
Yesu Alirira Mzinda Wa Yerusalemu 12.01.2024
Yesu Aphunzitsa Kupyolera M’mafanizo Osiyana Siyana Komanso Adalitsa Wana 11.01.2024
Yesu Alangiza Wophunzira Onse 10.01.2024
Fanizo La Kapitawo Wonyenga Ndi Yankho La Yesu Kwa Afarisi 09.01.2024
Yesu Akuphunzitsa Kudzera M’mafanizo A Nkhosa Yosokera, Ndalama Yotayika, Ndi Wana Awiri Wolowerera 08.01.2024
Yesu Aphunzitsa Kudzera M’mafanizo Osiyana-Siyana 05.01.2024
Yesu Akupitiliza Kuphunzitsa Ndi Kuchilitsa Pa Ulendo Waku Yerusalemu 04.01.2024
Yesu Aphunzitsa Ndi Mafanizo Ambiri 03.01.2024
Yesu Aphunzitsa Za Pemphero Komanso Adzudzula Afarisi 02.01.2024
Fanizo La Msamariya Wachifundo 01.01.2024
Ulendo Wa Yesu Ku Yerusalemu 29.12.2023
Yesu Aphunzitsa Kudzera M’mafanizo 28.12.2023
Machilitso, Kuukitsa Akufa Ndi Kuyamikira Yohane M’batizi 27.12.2023
Kusankha Ophunzira Khumi Ndi Awiri Ndi Chiphunzitso Chapachigwa 26.12.2023
Yesu Asankha Ophunzira, Achiritsa Ndi Kuphunzitsa 25.12.2023
Yesu Akanidwa Ndi Abale Wake 22.12.2023
Yohane M’batizi; Kuunika Muzu WaMariya, Komanso Kuyesedwa Kwa Yesu 21.12.2023

Ouça o podcast TTB Chichewa no Replaio

Rádio e podcasts em um só app - grátis e sem cadastro. Instale hoje e não perca o lançamento

Baixe no Google Play

O Replaio não é o publicador dos podcasts; os nomes dos programas, as capas e o áudio pertencem aos seus autores e são distribuídos por feeds RSS públicos