Thru the Bible Chichewa

TTB Chichewa

Pologalamu ya Tisanthule Baibulo ndi gawo limodzi lautumiki, ophunzitsa Baibulo, otchedwa ulendo m??baibulo (Thru the Bible). Mndandanda wamapogalamuwu unakonzedwa ndi Dr. J. Vernon McGee ndipo unatanthauzidwa mu zilankhulo zoposa zana zimodzi (100). Zinakonzedwa kuti pologalamu imodzi idzikhala ya mphindi makumi atatu (30) ndipo kuti pomaliza zidzathe kuthandiza omvera kumvetsetsa Baibulo lonse. Ndipo pakali pano mapologalamu onsewa tawaika pamakina a Intaneti. Ndife oyamika kuti mwasankha kuphunzira zambiri zokhudza mau a Mulungu kudzera mmapologalamuwa. Tikukulimbikitsani kuti mudzimvera po...

Não deixe de visitar o site do podcast e apoiar quem o produz: ttb.twr.org

Autor

Thru the Bible Chichewa

Categoria

Religion

Site do podcast

ttb.twr.org

Último episódio

30 de out de 2024

Onde ouvir?

Podcasts no app Replaio Radio Em breve

Os podcasts estão chegando ao app. Instale agora e seja o primeiro a descobrir um jeito totalmente novo de curtir podcasts

Baixe no Google Play Instale grátis Android 5 mi+ downloads · nota 4,8 iOS em breve

Episódios

Mulungu Athana Ndi Kugalukira Ndi Kusamvera 15.11.2023
Ntchito Ya Tsiku Ndi Tsiku Ya Ansembe 14.11.2023
Kupatulika Kwa Ansembe 13.11.2023
Nsembe Yopalamula Ndi Nsembe Ya Mtendere 10.11.2023
Kuunika Za Nsembe Yopalamula 09.11.2023
Zochimwa Za Mtundu Wonse Wa Israyeli, Mtsogoleri Ndi Anthu Wamba 08.11.2023
Nsembe Ya Uchimo Pochimwa Wansembe 07.11.2023
Nsembe Ya Mtendere 06.11.2023
Nsembe Ya Ufa Ndi Ya Zipatso Zoyamba 03.11.2023
Malamulo, Mwambo Ndi Chifukwa Chopereka Yopsereza 02.11.2023
Chiyambi Cha Bukhu La Levitiko Ndi Za Nsembe Yopsereza 01.11.2023

Ouça o podcast TTB Chichewa no Replaio

Rádio e podcasts em um só app - grátis e sem cadastro. Instale hoje e não perca o lançamento

Baixe no Google Play

O Replaio não é o publicador dos podcasts; os nomes dos programas, as capas e o áudio pertencem aos seus autores e são distribuídos por feeds RSS públicos