Thru the Bible Chichewa

TTB Chichewa

Religion EN ↓ 261 episodes

Pologalamu ya Tisanthule Baibulo ndi gawo limodzi lautumiki, ophunzitsa Baibulo, otchedwa ulendo m??baibulo (Thru the Bible). Mndandanda wamapogalamuwu unakonzedwa ndi Dr. J. Vernon McGee ndipo unatanthauzidwa mu zilankhulo zoposa zana zimodzi (100). Zinakonzedwa kuti pologalamu imodzi idzikhala ya mphindi makumi atatu (30) ndipo kuti pomaliza zidzathe kuthandiza omvera kumvetsetsa Baibulo lonse. Ndipo pakali pano mapologalamu onsewa tawaika pamakina a Intaneti. Ndife oyamika kuti mwasankha kuphunzira zambiri zokhudza mau a Mulungu kudzera mmapologalamuwa. Tikukulimbikitsani kuti mudzimvera po...

Be sure to visit the podcast's website and support the creator: ttb.twr.org

Author

Thru the Bible Chichewa

Category

Religion

Podcast website

ttb.twr.org

Latest episode

Oct 30, 2024

Where to listen?

Podcasts in the app Replaio Radio Coming soon

Podcasts are coming to the app soon. Install now and be the first to see a whole new take on podcasts

Get it on Google Play Install for free Android almost 10M downloads · 4.8 rating iOS soon

Episodes

Mulungu Aitana Barnaba Ndi Paulo; Zochitika Ku Kupro; Marko Abwerera Ndi Zochitika Ku Antiokeya 17.07.2024
Petulo Atuluka Mndende, Paulo Ndi Banaba Abwelera Ku Antiyokeya 16.07.2024
Mau A Petro Odziteteza Pophatikana Ndi Anthu A Amitundu Komanso Tiona Za Mpingo Wa Ku Antiokeya 15.07.2024
Chipulumutso Cha A Amitundu Chikudza Ndi Mphamvu Ya Mulungu 12.07.2024
Kutembenuka Mtima Kwa Saulo; Utumiki Wa Petro Ku Yopa Ndi Luda 11.07.2024
Filipo Athandiza Mdindo Wa Ku Aitiopiya Kutembenuka Mtima 10.07.2024
Masautso Akulu; Utumiki Wa Filipo; Chikhulupiriro Cha Simoni; Utumiki Wa Petro Ndi Yohane; Mlaliki Filipo 09.07.2024
Kudzikanila Kwa Stefano Pamaso Pa Bwalo La Sanhedrin Ndi Imfa Yake 08.07.2024
Udani Wa M’chikhalidwe; Kuyendetsa Mpingo Moopa Mulungu; Kukula Kwa Mpingo Muyerusalemu; Ndi Kuona Adani A Stefano 05.07.2024
Kuchotsa Chodetsa Mumpingo; Kufalitsa Uthenga Kopambana Ndi Kuzunzika Kwa Mpingo Ndi Upangiri Wa Gamalieli 04.07.2024
Kusakondwa Kwa Atsogoleri A Chiyuda Ndi Petro Ndi Yohane; Kuweruza Kwachilendo; Kuopseza; 03.07.2024
Mphamvu za Mzimu Woyera, Petulo alalikiranso 02.07.2024
Petulo ayankha otsutsana naye, Uneneri wa Yoeli; Petulo alalika Yesu anthu 3,000 nkutembenuka mtima 01.07.2024
Kuyamba kwa mpingo komanso ubatizo wa Mzimu Woyera 28.06.2024
Yesu alangiza Ophunzira ake, alonjeza mzimu woyera komanso za kukwera kwake 27.06.2024
Mlatho komanso Mbiri ya bukhu 26.06.2024
Rute mumtima komanso pakhomo la Boazi 25.06.2024
Rute asankha Boazi ngati mlowamalo 24.06.2024
Rute kukunkha kwa Boazi 21.06.2024
Rute Apitiliza Kukunkha Chakudya M’munda Wa Boazi 20.06.2024
Rute Akunkha Chakudya M’munda Wa Boazi 19.06.2024
Kubwerera ku Betelehemu 18.06.2024
Chiyambi, Kulowa ku Moabu 17.06.2024
Dziko lilowerera pauzimu ndi pa ndale 14.06.2024
Oweruza Samusoni 13.06.2024

Listen to the TTB Chichewa podcast in Replaio

Radio and podcasts in one app - free, with no sign-up. Install today and do not miss the launch

Get it on Google Play

Replaio is not a podcast publisher; show names, artwork and audio belong to their authors and are distributed through public RSS feeds.