Thru the Bible Chichewa

TTB Chichewa

Religion EN ↓ 261 episodes

Pologalamu ya Tisanthule Baibulo ndi gawo limodzi lautumiki, ophunzitsa Baibulo, otchedwa ulendo m??baibulo (Thru the Bible). Mndandanda wamapogalamuwu unakonzedwa ndi Dr. J. Vernon McGee ndipo unatanthauzidwa mu zilankhulo zoposa zana zimodzi (100). Zinakonzedwa kuti pologalamu imodzi idzikhala ya mphindi makumi atatu (30) ndipo kuti pomaliza zidzathe kuthandiza omvera kumvetsetsa Baibulo lonse. Ndipo pakali pano mapologalamu onsewa tawaika pamakina a Intaneti. Ndife oyamika kuti mwasankha kuphunzira zambiri zokhudza mau a Mulungu kudzera mmapologalamuwa. Tikukulimbikitsani kuti mudzimvera po...

Be sure to visit the podcast's website and support the creator: ttb.twr.org

Author

Thru the Bible Chichewa

Category

Religion

Podcast website

ttb.twr.org

Latest episode

Oct 30, 2024

Where to listen?

Podcasts in the app Replaio Radio Coming soon

Podcasts are coming to the app soon. Install now and be the first to see a whole new take on podcasts

Get it on Google Play Install for free Android almost 10M downloads · 4.8 rating iOS soon

Episodes

Nsanje ya Efurayimu, za oweruza ena anatu 12.06.2024
Yefuta abweretsa chipambano kwa Amoni 11.06.2024
Utsogoleri wakanika 10.06.2024
Zaka 40 zamtendere pansi pa utsogoleri wa Gidiyoni 07.06.2024
Mulungu apulumutsa Israyeli kudzera mwa Gidiyoni 06.06.2024
Kulowelera kwa kachisanu ndi chimodzi 05.06.2024
Nyimbo ya Debora ndi Baraki 04.06.2024
Mulungu agwiritsa anthu wamba kupulumutsa Israyeli 03.06.2024
Zochitika ku Israyeli atamwalira Yoshua 31.05.2024
Uthenga womaliza wa Yoshuwa 30.05.2024
Midzi Ya A Levi Ndi Midzi Iwiri Ya Hafu Ikhala Kum’mawa Kwa Yordano 29.05.2024
Kumaliza Kugawa Madera Kwa Ana A Israyeli Ndi Midzi Yopulumukiramo 28.05.2024
Kudula Malire A Malo A Mapfuko Ya Ana A Israyeli 27.05.2024
Dziko La Kum’mawa Kwa Mtsinje Wa Yordano Ndi Gawo La Kalebe 24.05.2024
Kutsiriza Nkhondo Ya Kum’mwera Ndi Kupita Kumpoto Kwa Kanani 23.05.2024
A Gibeoni Ndi Nkhondo Yochokera Kum’mwera 22.05.2024
Israyeli Alephera kugonjetsa Ai Kenaka Tiona Kupasuka kwake 21.05.2024
Kugonjetsa Mudzi Wa Yeriko 20.05.2024
Zinthu Zitatu Zochitika Komanso Zofunika Kwambiri 17.05.2024
Israyeli Aoloka Mtsinje Wa Yordano 16.05.2024
Yoswa Atenga Ulamuliro Pa Israyeli 15.05.2024
Chiyambi Cha Bukhu La Yoswa, Yoswa Atenga Udindo Ndi 14.05.2024
Nyimbo Ya Mose, Mdalitso Ndi Imfa Yake Ulamuliro Wake 13.05.2024
Moyo Ndi Zabwino Kulinganiza Ndi Imfa Ndi Zoyipa; Kusintha Kwa Utsogoleri 10.05.2024
Pangano La Dziko La Malonjezano 09.05.2024

Listen to the TTB Chichewa podcast in Replaio

Radio and podcasts in one app - free, with no sign-up. Install today and do not miss the launch

Get it on Google Play

Replaio is not a podcast publisher; show names, artwork and audio belong to their authors and are distributed through public RSS feeds.