Thru the Bible Chichewa

TTB Chichewa

Religion EN ↓ 261 episodes

Pologalamu ya Tisanthule Baibulo ndi gawo limodzi lautumiki, ophunzitsa Baibulo, otchedwa ulendo m??baibulo (Thru the Bible). Mndandanda wamapogalamuwu unakonzedwa ndi Dr. J. Vernon McGee ndipo unatanthauzidwa mu zilankhulo zoposa zana zimodzi (100). Zinakonzedwa kuti pologalamu imodzi idzikhala ya mphindi makumi atatu (30) ndipo kuti pomaliza zidzathe kuthandiza omvera kumvetsetsa Baibulo lonse. Ndipo pakali pano mapologalamu onsewa tawaika pamakina a Intaneti. Ndife oyamika kuti mwasankha kuphunzira zambiri zokhudza mau a Mulungu kudzera mmapologalamuwa. Tikukulimbikitsani kuti mudzimvera po...

Be sure to visit the podcast's website and support the creator: ttb.twr.org

Author

Thru the Bible Chichewa

Category

Religion

Podcast website

ttb.twr.org

Latest episode

Oct 30, 2024

Where to listen?

Podcasts in the app Replaio Radio Coming soon

Podcasts are coming to the app soon. Install now and be the first to see a whole new take on podcasts

Get it on Google Play Install for free Android almost 10M downloads · 4.8 rating iOS soon

Episodes

Sauli Agonjetsa Amoni Ndi Kuchoka Kwa Udindo Kwa Samueli Kupita Kwa Sauli 21.08.2024
Sauli Asankhidwa Ndi Kudzozedwa 20.08.2024
Chilango Cha Mulungu Pa Afilisti; 19.08.2024
Kuitanidwa Kwa Samueli; Chilango Cha Mulungu Pa Eli Ndi Ana Ake Chikwanitsidwa; Komanso Chilango Cha Mulungu Pa Afilisti 16.08.2024
Pemphero La Hana La Ulosi; Ana A Eli Woipa; Mwana Samueli M’kachis 15.08.2024
Chiyambi Cha Bukhuli, Kubadwa Kwa Samueli 14.08.2024
Chifundo Cha Anthu Akunja Machilitso Ya Yesu; Ulendo Wotsiriza Ku Roma Ndi Ayuda 13.08.2024
Ulendo Wa Paulo Wamasautso Ukuptilira Panyanja Paoneka Mwera Ndi Kuonongeka Kwa Ngalawa 12.08.2024
Paulo Atsika Ku Kaisareya Ndi Kuyamba Ulendo Wake Wa Pa Nyanja Wopita Ku Roma 09.08.2024
Masautso A Paulo Akupitilira Pa Ulendo Wake Wa Ku Roma, Kuchitira Umboni Uitanidwa Ku Kaisareya 08.08.2024
Ulendo Woopsa Wa Paulo Ukupitilira Ndi Umboni Ku Kaisareya 07.08.2024
Ulendo Woopsa Wa Paulo Ku Roma Ukupitilira 06.08.2024
Ulendo Woopsa Wa Paulo Ku Roma Ukupitirira 05.08.2024
Zobvuta Zokonzedwa Ndi A Yuda Zikupitilira Pa Ulendo Wa Paulo Ku Aroma 02.08.2024
Ulendo Wamasautso Wa Paulo Ku Roma 01.08.2024
Maulendo A Paulo, Zochenjeza Kwa Paulo Ndi Kuti Akhala Ndi A Yuda 31.07.2024
Utumiki Wa Paulo Ndi Umboni Wake Kwa Akulu Ku Efeso 30.07.2024
Utumiki Wa Paulo Uchita Bwino Pa Zaka Ziwiri Mu Efeso; Gulu La Oukira Ndimlembi Abwino; Paulo Apita Ku Greece Ndi Ku Korinto 29.07.2024
Paulo Ku Korinto Ndi Bvuto La Ayuda; Nthawi Pang’ono Ku Aefeso; Ulendo Wachitatu Wa Paulo 26.07.2024
Paulo Alalikira Ku Atene Mkati 25.07.2024
Uthenga Wabwino Ulandiridwa Ku Atesalonika Ndi Ku Berea; Ayuda 24.07.2024
Paulo; Kuitanidwa Ku Ulaya Ndi Zochitika Ku Afilipi 23.07.2024
Gawo La Chiwiri Loona Ngati M’dulidwe Ndi Lamulo La Mose Ndizofunika Kapena Ayi; Komanso Paulo Ndi Barnaba Apatukana 22.07.2024
Gawo Loyamba La Loona Ngati Mdulidwe Ndi Lamulo La Mose Ndilofunika Kapena Ayi 19.07.2024
Uthenga Wabwino Ulalikidwa Ku Ikoniyo, Lustra, Ndi Derbe; Kubwereranso Ku Lustra Ndi Ikoniyo Ndi Antiokeya; Ndi Kubwerera Kunyumba 18.07.2024

Listen to the TTB Chichewa podcast in Replaio

Radio and podcasts in one app - free, with no sign-up. Install today and do not miss the launch

Get it on Google Play

Replaio is not a podcast publisher; show names, artwork and audio belong to their authors and are distributed through public RSS feeds.