Thru the Bible Chichewa

TTB Chichewa

Religion EN ↓ 261 episodes

Pologalamu ya Tisanthule Baibulo ndi gawo limodzi lautumiki, ophunzitsa Baibulo, otchedwa ulendo m??baibulo (Thru the Bible). Mndandanda wamapogalamuwu unakonzedwa ndi Dr. J. Vernon McGee ndipo unatanthauzidwa mu zilankhulo zoposa zana zimodzi (100). Zinakonzedwa kuti pologalamu imodzi idzikhala ya mphindi makumi atatu (30) ndipo kuti pomaliza zidzathe kuthandiza omvera kumvetsetsa Baibulo lonse. Ndipo pakali pano mapologalamu onsewa tawaika pamakina a Intaneti. Ndife oyamika kuti mwasankha kuphunzira zambiri zokhudza mau a Mulungu kudzera mmapologalamuwa. Tikukulimbikitsani kuti mudzimvera po...

Be sure to visit the podcast's website and support the creator: ttb.twr.org

Author

Thru the Bible Chichewa

Category

Religion

Podcast website

ttb.twr.org

Latest episode

Oct 30, 2024

Where to listen?

Podcasts in the app Replaio Radio Coming soon

Podcasts are coming to the app soon. Install now and be the first to see a whole new take on podcasts

Get it on Google Play Install for free Android almost 10M downloads · 4.8 rating iOS soon

Episodes

Kulephera Kwa Chiwembu Cha Adoniya; Solomoni Adzozedwa Mfumu; Malangizo A Davide Kwa Solomoni. 25.09.2024
Mau Otsiriza A Davide; Anyamata A Davide Amphamvu Ndi Chiwerengero 24.09.2024
Njala Mu Israyeli, Agibeoni Abwezera Nkhondo Ndi Afilisti 23.09.2024
Davide Abwezeretsedwa Pa Ufumu Wake Ndipo Seeba Aukira 20.09.2024
Nkhondo Pakati Pa Davide Ndi Absalomu 19.09.2024
Abisalomu Aukira Atate Wake, Davide 18.09.2024
Uchimo Wa Ana A Davide; Amoni Ndi Absalomo 17.09.2024
Natani Adzudzula Davide Chifukwa Cha Uchimo Wake Ndipo Davide Alapa Chimolo 16.09.2024
Davide Ayambana Ndi Ammoni Ndi Asuri Ndi Uchimo Uwiri Waukulu Wa Davide 13.09.2024
Ufumu Wa Davide Ukhala Wamphamvu Ndipo Davide Akhala Pa Ubwezi Ndi Mefiboseti 12.09.2024
Pangano La Mulungu Pa Kumanga Nyumba Ya Davide 11.09.2024
Njira Zoyenera Ndi Zolakwika Zomwe Davide Anatenga Pobweretsa Likasa Ku Yerusalemu 10.09.2024
Davide Akhazikitsidwa Mfumu Wa Israyeli Yense 09.09.2024
Davide Akhazikitsidwa Mfumu 06.09.2024
Sauli Ndi Jonatani Aphedwa Ku Nkhondo 05.09.2024
Moyo Wa Davide Pamene Ali Pakati Pa Afilisti 04.09.2024
Davide Abwerera Kudziko La Afilisti Pamene Sauli Apita Kwa Sing’anga 03.09.2024
Davide Akwatira Abigayeli Ndipo Davide Asiya Kupha Sauli Kachiwiri 02.09.2024
Chitetezo Ndi Chisamaliro Cha 30.08.2024
Davide Asonkhanitsa Anyamata 29.08.2024
Mulungu Alanga Davide; Ndipo Davide Apempha Ansembe Kuti Amuthandize 28.08.2024
Mulungu Akuphunzitsa Davide; Sauli Afuna Kupha Davide; Ndipo Jonatani Amuthandiza Kuthawa 27.08.2024
Davide Adzonzedwa Ndipo Akupha Goliati 26.08.2024
Kusamvera Kwa Sauli Pa Agagi Ndipo Samueli Mudzudzula 23.08.2024
Sauli Apandukira Mulungu; Yonatani Apambana Pankhondo Ya Afilisti; Komanso Kuipa Kwa Lamulo Lofulumira La Sauli 22.08.2024

Listen to the TTB Chichewa podcast in Replaio

Radio and podcasts in one app - free, with no sign-up. Install today and do not miss the launch

Get it on Google Play

Replaio is not a podcast publisher; show names, artwork and audio belong to their authors and are distributed through public RSS feeds.