Thru the Bible Chichewa

TTB Chichewa

Pologalamu ya Tisanthule Baibulo ndi gawo limodzi lautumiki, ophunzitsa Baibulo, otchedwa ulendo m??baibulo (Thru the Bible). Mndandanda wamapogalamuwu unakonzedwa ndi Dr. J. Vernon McGee ndipo unatanthauzidwa mu zilankhulo zoposa zana zimodzi (100). Zinakonzedwa kuti pologalamu imodzi idzikhala ya mphindi makumi atatu (30) ndipo kuti pomaliza zidzathe kuthandiza omvera kumvetsetsa Baibulo lonse. Ndipo pakali pano mapologalamu onsewa tawaika pamakina a Intaneti. Ndife oyamika kuti mwasankha kuphunzira zambiri zokhudza mau a Mulungu kudzera mmapologalamuwa. Tikukulimbikitsani kuti mudzimvera po...

Não deixe de visitar o site do podcast e apoiar quem o produz: ttb.twr.org

Autor

Thru the Bible Chichewa

Categoria

Religion

Site do podcast

ttb.twr.org

Último episódio

30 de out de 2024

Onde ouvir?

Podcasts no app Replaio Radio Em breve

Os podcasts estão chegando ao app. Instale agora e seja o primeiro a descobrir um jeito totalmente novo de curtir podcasts

Baixe no Google Play Instale grátis Android 5 mi+ downloads · nota 4,8 iOS em breve

Episódios

Kupitiliza Kuphunzitsa Za Mzimu Woyera 03.04.2024
Yesu Achenjeza Za Kubwera Kwa Otsutsa 02.04.2024
Wophunzira Ayenera Kukhala Mwa Yesu Ndi Kumumvera Iye 01.04.2024
Yesu Adzitchula Kukhala Mpesa Ndipo Ophunzira Ake Ndiwo Nthambi 29.03.2024
Yesu Alonjeza Mzimu Woyera 28.03.2024
Yesu Alimbikitsa Ophunzira Wake 27.03.2024
Yudase Achoka Ndipo Yesu Aneneratu Kuti Petro Adzamukana Iye 26.03.2024
Yesu Asambitsa Mapazi Ya Ophunzira Ake 25.03.2024
Yesu Alowa M’nthawi Ya Masautso 22.03.2024
M’yuda Ndi Ahelene Achitira Yesu Umboni 21.03.2024
Yesu Aukitsa Lazaro Kwa Akufa 20.03.2024
Yesu Akonzekeretsa Ophunzira Wake Kuti Akumane Ndi Lazaro 19.03.2024
Yesu Akudziula Kuti Ndiye M’busa Wabwino 18.03.2024
Israyeli Akuonetsa Chithunzi Chakuti Ndikhola La Nkhosa 15.03.2024
Munthu Wosaona Uja, Tsopano Waona Yesu 14.03.2024
Yesu Atsegula Maso A Munthu Amene Anabadwa Ali Wakhungu 13.03.2024
Yesu Akudziulura Kuti Ndiye Kuunika Kwa Dziko Lapansi 12.03.2024
Yesu Akhulukira Mkazi Wogwidwa Chigololo 11.03.2024
Udani Ukukula Pa Yesu 08.03.2024
Yesu Apitiliza Kuphunzitsa Za Mkate Wamoyo 07.03.2024
Yesu Adziulula Kuti Ndiye Mkate Wa moyo 06.03.2024
Yesu Adyetsa Anthu Zikwi Zisanu (5,000) Komanso Ayenda Pa Nyanja 05.03.2024
Yesu Atsimikiza Kunena Kuti Iye Ndi Atate Wake, Ali Amodzi 04.03.2024
Yesu Aulura Umulungu Wake Ndipo Ayuda Atsutsana Naye 01.03.2024
Chipulumutso M’mudzi Wa Samariya 29.02.2024

Ouça o podcast TTB Chichewa no Replaio

Rádio e podcasts em um só app - grátis e sem cadastro. Instale hoje e não perca o lançamento

Baixe no Google Play

O Replaio não é o publicador dos podcasts; os nomes dos programas, as capas e o áudio pertencem aos seus autores e são distribuídos por feeds RSS públicos