Thru the Bible Chichewa

TTB Chichewa

Pologalamu ya Tisanthule Baibulo ndi gawo limodzi lautumiki, ophunzitsa Baibulo, otchedwa ulendo m??baibulo (Thru the Bible). Mndandanda wamapogalamuwu unakonzedwa ndi Dr. J. Vernon McGee ndipo unatanthauzidwa mu zilankhulo zoposa zana zimodzi (100). Zinakonzedwa kuti pologalamu imodzi idzikhala ya mphindi makumi atatu (30) ndipo kuti pomaliza zidzathe kuthandiza omvera kumvetsetsa Baibulo lonse. Ndipo pakali pano mapologalamu onsewa tawaika pamakina a Intaneti. Ndife oyamika kuti mwasankha kuphunzira zambiri zokhudza mau a Mulungu kudzera mmapologalamuwa. Tikukulimbikitsani kuti mudzimvera po...

Não deixe de visitar o site do podcast e apoiar quem o produz: ttb.twr.org

Autor

Thru the Bible Chichewa

Categoria

Religion

Site do podcast

ttb.twr.org

Último episódio

30 de out de 2024

Onde ouvir?

Podcasts no app Replaio Radio Em breve

Os podcasts estão chegando ao app. Instale agora e seja o primeiro a descobrir um jeito totalmente novo de curtir podcasts

Baixe no Google Play Instale grátis Android 5 mi+ downloads · nota 4,8 iOS em breve

Episódios

Malonjezo A Mulungu; Madalitso Pakumvera Ndi Tsoka Pa kusamvera 08.05.2024
Kukwapula Wolakwa, Kuteteza Mkazi Wamasiye, Chilango Cha Amaleke, Ndi Chopereka Cha Zipatso Zoyamba 07.05.2024
Kukhala Mu Israyeli, Ukhondo, Malamulo A Mose Pa Kuthetsa Ukwati Ndi Malamulo Wena 06.05.2024
Chilango Chopachikidwa Pamtengo; Za 03.05.2024
Malamulo A Nkhondo, Kupha, Amayi 02.05.2024
Mesiya, Mneneri Woona Ndi Onama, Midzi Yopulumikira Ndi Malamulo Wena 01.05.2024
Kumtumikira Mulungu Ndi Mtima Wonse; 30.04.2024
Chaka Chopuma, Ukapolo, Madyerero Atatu, Kuweruza Ndi Kupembedza Mafano 29.04.2024
Kupitiliza Za Aneneri Onama; Midzi Yonyasa; Chikhalidwe Ndi malamulo apa Chakudya ndi chakhumi 26.04.2024
Lamulo Lakutenga Malo, Malo Amodzi Opembedzerapo, Malamulo A Zakudya Ndi Kuchenjeza Za Aneneri Onama 25.04.2024
Kulephera Kwa Israyeli; Miyala Ya Malamulo Atsopano; Kupembedzera Kwa Mose; Kupatulidwa Kwa A Levi; Chisamaliro Cha Mulungu; Ndi Lamulo La Kutenga Malo 24.04.2024
Zomwe Anachita Mulungu M’mbuyomo, Ndizimene Zimapereka Chilimbikitso Pa Zomwe Mulungu Adzachite 23.04.2024
Chipulumutso Ndiubale Omwe 22.04.2024
Mose Apereka Ndi Kumasuliranso Malamulo 19.04.2024
Chikondi Cha Mulungu Chionekera Mwa Isarayeli Ndipo Ayenera Kuphunzitsa Ana Kupembedza Mulungu M’mzimu 18.04.2024
Mose Aunikanso Za Kulephera Kwa Israyeli M’njira Zosiyana-Siyana Ndipo awalimbikitsa Kuti Amvere Mulungu 17.04.2024
Chiyambi Cha Bukhu La Deuterenomo Ndi Kuona Za Uchimo WaIsrayeli Pa Kadesi Barnea 16.04.2024
Mau Omaliza A Yohane Otseka Nawo Bukhu 15.04.2024
Ophunzira Aona Yesu Atauka Kumanda 12.04.2024
Kuuka Ku Manda Kwa Yesu Kristu 11.04.2024
Imfa Ya Yesu Pa Mtanda 10.04.2024
Yesu Kubwalo La Annasi Ndi Pilato 09.04.2024
Yesu Agwidwa M’munda Wa Getsemane 08.04.2024
Yesu Apempherera Ophunzira Wake M’nyengo Yonse 05.04.2024
Yesu Apenya Mtsogolo Ndi Chiyembekezo Cha Mtanda 04.04.2024

Ouça o podcast TTB Chichewa no Replaio

Rádio e podcasts em um só app - grátis e sem cadastro. Instale hoje e não perca o lançamento

Baixe no Google Play

O Replaio não é o publicador dos podcasts; os nomes dos programas, as capas e o áudio pertencem aos seus autores e são distribuídos por feeds RSS públicos