Gospel Life
Chiphunzitso Choona | Sound Doctrine
Sermons and teaching in Chichewa and English
Author
Gospel Life
Category
Podcast website
Latest episode
Apr 24, 2026
Where to listen?
Podcasts in the app Replaio Radio Coming soonPodcasts are coming to the app soon. Install now and be the first to see a whole new take on podcasts
Episodes
Jesus the lord of History, the lord of the world 05.09.2022 54:56
Maliko 6:30-44, M'ma vesi amenewa tikuonetseredwa bwino lomwe za m'momwe mbiri m'baibulo ikuonetsera dongosolo lomwe Mulungu analikonza kale lokhuza kubwera kwa khristu pa dziko lapansi kuzapulumutsa anthu ake. Mwachitsanzo, aneneri angapo akutengeredwa ku malo, kapena akupita kumalo omwe kulibeko chakudya kapena chakudyacho ndichochepa. Aneneri monga Mose, Eliya ndi ena otero, pomwe izi zikuwachi...
Mulungu Avumbulutsa Chilungamo ndi Chisomo chake/God reveals his Justice and Grace 03.08.2022 41:55
Genesis 7:1-10, Mmavesi amenewa tikuphunzira za chenjezo lomwe lina pelekedwa munthawi ya Nowa pomwe anthu ankangodya, kumwa, kukwatira ndi kukwatiwa kufikira Nowa analowa mchombo ndipo chigumula chinabwera. Zomwe ndi chimodzimodzi munthawi yathu lero, pomwe anthu akungodya, kumwa, kukwatira ndi kukwatiwa. Panthawi yomweyo tikuona za kulungama kwa Nowa komwe kwabwera chifukwa chachikhulupiriro cha...
Nowa ndi chigumula/Noah and the flood 26.07.2022 54:17
Genesis 6:9-22, chiwawa chinadzadza pa dziko lapansi kotero kuti dziko linakhala lowonongeka pamaso pa Mulungu. Izi zinapangisa Mulungu kutsindikadi kwa Nowa kuti sachitiranso mwina koma kuliwononga dziko lapansi ndi zamoyo zonse. Koma Nowa anali munthu wolungama ndiwopanda tchimo pakati pa anthu a m'bado wake. Ndipo Nowa anayenda ndi Mulungu. Genesis 6:9-22, But the earth had become ruined in the...
Yehova akomera mtima Nowa/Jehovah favours Noah 19.07.2022 20:53
Genesis 6:5-8, Kuyipa kwa munthu pa dziko la pansi kumakulirakulirabe ndikuti nthawi zonse amalingalira ndikukhumbira kuchita zoyipa zokhazokha, Yehova anamva chisoni kuti analenga munthu ndikumuyika pa dziko lapansi, ndipo anawawidwa mtima. Genesis 6:5-8, Consequently ,Jehovah saw that man's wickedness was great on the earth and that every inclination of the thoughts of his heart was only bad all...
Kuyipa kwakulu kwa anthu 11.07.2022 1:00:24
Genesis 6:1-4, ikulongosola za chiyambi chachionongeko cha dziko la pansi ndi chilengedwe chonse chimene Mulungu anachilenga. Mulungu akuononga chilengedwe chonse chomwe anachilenga chifukwa chakuti chilengedwecho (Anthu) chamukana Mulungu. Genesis 6:1-4, these verses are basically focusing the discussion on the cause of the destruction of the world and its creation. God is rejected by his creatio...
Banja la Kaini ndi Mbewu ya mzimayi 04.07.2022 52:13
Genesis 4:17-26, ikukamba za banja la Kaini komanso kubweresa poyera kupitirira kwa kusamvera kwa Kaini ndi mtundu wake wonse. Izi zili chomwecho pomwe tikuwona Lameki akukwatira akazi awiri motsutsana ndi dongosolo la ukwati lomwe Mulungu analikhadzikitsa kuti mwamuna akuyenera kukwatira mkazi m'modzi. Panthawi yomweyo tikuwonanso zokhuza mbewu ya mzimayi yomwe ikubwera kudzera mwa Seti yemwe aku...
Mdalitso wochokera kwa Mulungu kupita kwa ana a Adamu ndi Zotsatira zake/Blessings from God upon Adam's children and their response. 21.06.2022 1:10:59
Mulungu akudalitsa Kaini komanso Abele panthawi yomwe agwira ntchito zawo ndipo iwo akulandira zotsatira zabwino kuchokera ku ntchito zawozi. Panthawi yomweyo tikuona kuthokoza kosiyana komwe kukubwera kuchokera kwa anthu awiriwa omwe agwira ntchito zosiyana pomwe apeleka nsembe zawo kwa Mulungu. God blesses Cain and Abel when doing their separate work and are blessed abundantly while on the other...
Chilungamo ndi Chisomo Adam ndi Hava atachimwa |Justice and Grace after the fall 13.06.2022 48:23
Genesis 3:17-24, mu uthenga uwu tikuona chilungamo cha mulungu chikuonetsedwa chifukwa cha kusamvera kwa Adamu, komanso tikuona mulungu akupeleka chisomo kwa Adamu chifukwa cha chikhulupiriro chake. Chilungamo cha mulungu chinaonekera mu chilango chomwe chinapelekedwa kwa Adamu chifukwa cha tchimo lake. M'dzanja linali tikuona mulungu akuonetsa chisomo kwa Adamu pamene anakhulupirira malonjedzo a...
Chulukitsani Alimi | Multiply Farmers 02.12.2020 21:18
Pamene tapanga ophunzira, tiziyembekezera ophunzira atsopano kupanganganso ophunzira ochuluka. Pamene tawazindikira, tikuyenera kuwaphunzitsa komanso kuwatumiza ophunzira atsopanowa. Tikatero timakhala kuti tatumiza alimi ochulukira m’minda ku ntchito yodzala mipingo. When we make disciples, we should expect new disciples to make more disciples. When we identify, invest in, and send out these new...
Kololani m’Munda | Harvest the Field 02.12.2020 29:53
Pamene talalikira uthenga wabwino ndikuphunzitsa okhulupirira atsopano, ndi nthawi yoti tiwakhonzekeretse okhulupirira atsopano kuti akhale mpingo. Mpingo umakhala ndi anthu omwe ndi ziwalo ndipo amasonkhana pamodzi kuti amve ulaliki wa baibulo. Mpingowo umachita ubatizo ndi mgonero wa ambuye ndipo umatsogozedwa ndi abusa ndi atumiki. After we have preached the gospel and discipled new believers,...
Samalirani m’Munda | Tend the Field 02.12.2020 22:22
Monga munda omwe wayamba kukula, akhirisitu atsopano amafunika chisamaliro chauzimu pafupipafupi. Yesu akutilamula kuti tibatize wokhulupirira atsopano ndi kuwaphunzitsa malamulo ake. Like a field that has started to grow, new Christians need constant spiritual care. Jesus commands us to baptize new believers and to teach them his commands.
Dzalani m'Munda | Sow the Field 02.12.2020 19:46
Kudzala kachisi wa tsopano kuchokera mubaibulo, tikuyenera kudzala munda ndi mbewu ya uthenga wa wabwino. Izi zimafunika kuti tifalitse uthenga wa bwino momveka bwino komanso kwa anthu ambiri. Pamene tifalitsa uthenga wa mulungu, Yesu akutiuza kuti tiyembekeze mayankho anayi (Marko 4:11-20). To biblically plant a new church, we must sow the field with the seed of the gospel. This requires us to pr...
Limani m'Munda | Prepare the Field 02.12.2020 27:09
Timakhonza munda watsopano wodzalapo mpingo kudzera mupemphero. Timamupempha Mulungu kuti akonzekeretse nthaka yoti ilandire mbewu ya uthenga wa bwino. Koma tikuyeneranso kuzikonzekeretsa tokha popanga kafukufuku wa munda, kufunafuna munthu wamtendere, ndi kupanga ndondomeko zokaphunzitsa uthenga wabwino. We prepare a new field for church planting through prayer. We ask God to prepare the soil to...
Minda Inayi | The Four Fields 02.12.2020 21:05
Cholinga chathu ndikupanga ophunzira ndipo timapanga ophunzira polalikira uthenga wabwino ndi kudzala mipingo. Kuti tidzale mpingo timayenera kukonza munda, kudzala mmunda, kusamalira munda kenaka kukolola mmunda. Our goal is to make disciples, and we make disciples by sharing the gospel and planting churches. To plant churches, we must prepare the field, sow the field, tend the field, and then ha...
Pirirani Mpaka Kumapeto | Endure to the End 02.12.2020 28:46
Akolose 3:4; Yakobo 1:2-4. Imfa ya Yesu siikutitsimikizira kupindula. Akhirisitu amavutika. Koma kuvutika kumeneku ndi kuyesedwa kwa chikhulupiliro chawo. Iwo amene amakhulupiliradi sangataye chiphulumutso chawo konse, komano chikhulupiliro choonadi chimazindikirika pamene akhalabe okhulipirika mpaka kumapeto. Colossians 3:4; James 1:2–4. Jesus’ death does not guarantee us prosperity. Christ...
Vulani Chikhalidwe cha Uchimo | Take Off Sin 02.12.2020 26:29
Akolose 3:5-10; 1Yohane 1:5-9; Marko 7:21-23; Yakobo 1:14-15. Ana a Mulungu si a ngwiro. Amatha nthawi zina kuchimwa koma ana a Mulungu amavomereza matchimo awo ndipo amafunafuna kupha machimo awo kuchokera ku mizu po khonzanso malingaliro awo ndikuvala munthu watsopano. Colossians 3:5–10; 1 John 1:5–9; Mark 7:21–23; James 1:14–15. Children of God are not perfect. They do sometimes sin. But Childr...
Kutsindikizidwa ndi Mzimu Woyera 05.08.2020 36:59
Mulungu watitsindikiza ndi Mzimu Woyera kutitsimizira kuti chipulumutso chathu ndi chamuyaya. Komanso kuti madalitso onse achipulumutso athu tizalandi kutsogolo.
Kupembeza Limodzi ndi Banja | Worship with Family 05.08.2020 24:24
Akolose 3:18–21; Yoswa 24:15; Deuteronomo 6:6–9. Pamene Mulungu anakupangani kukhala atsopano, anayamba kupanga banja lanu kukhanso latsopano. Pangani Mulungu ku khala Mulungu wa banja lanu kudzera mukupembeza kwa banja. Colossians 3:18–21; Joshua 24:15; Deuteronomy 6:6–9. When God made you new, he began to make your family new. Make God the God of your home through family worship.
Kondani Anthu Ena | Love Others 05.08.2020 27:52
Akolose 3:12–13; Yohane 13:34–35. Dziko lidzadziwa kuti ndife ana aMulungu kudzera mu chikondi chathu. Baibulo likutilamulira ife kuti tikonde Mulungu, anasi utuu, wina ndi m'dzake, adani athu, komanso iwu omwe ndi osowa. Colossians 3:12–13; John 13:34–35. The world will know we are children of God by our love. The Bible commands us to love God, neighbor, one another, enemies, and those in need.
Kuchita Umboni wa Yesu | Witness about Jesus 27.05.2020 23:07
Akolose 3:1–4; 4:5–6; Machitidwe 1:8. Mulungu akuyitana mKhristu wina aliyense kukhala mboni ya Yesu. Kuchitira umboni wokhudzana ndi Yesu ndi kosavunga monga kuyakhula nkhani yako ndi nkhani ya Mulungu. Colossians 3:1–4; 4:5–6; Acts 1:8. God calls every Christian to be a witness about Jesus. Witnessing about Jesus is as easy as telling your story and telling God's story. Preacher: Dr. Joshua Hutc...
Perekani ku Mpingo Wanu | Give to Your Church 24.05.2020 21:07
Machitidwe 2:45; 2 Akorinto 9. Timapereka chifukwa Mulungu anatipatsa ife Mwana wake. Tikuyenera kukhala ndi dogosolo la kupereka kwathu komanso tikuyenera kupeka wokondwera. Acts 2:45; 2 Corinthians 9. We give because God gave us his Son. We need to plan our giving and to give cheerfully. Preacher: Dr. Joshua Hutchens Class: Kukhala Wophunzira: Kukhala Moyo Wosinthika ndi Uthenga Wabwino | Discip...
Imfa, Chiwukitso komanso Mapemphero a Yesu Khristu Tsopanolingo 21.05.2020 1:14:50
Oyera mtima apirira muchikhulupiriro chawo chifukwa imfa ya Yesu yachotsa chostutsa china chilichonse komanso mlandu uliwonse otsutsana ndi sosakhidwa a Mulungu. Chiukitso cha Yesu ndi chitsimikizo cha chikhulupiriro chathu komanso mpemphero ake opemperera oyera mtima amatsimikizira kuti chikhulupiriro cho sichifowoka. Preacher: Isaac Dzimbiri Class: Kudzama Choonadi Series: Kupirira kwa Oyera Mti...
Sonkhani Pamodzi kuti Mupembeze | Gather for Worship 19.05.2020 30:36
Machitidwe 2:42; Ahebri 10:24–25. Timasokhana pamodzi kuti tipembeze ndi cholinga choti tithandizone wina ndi nzake kukula musinkhu mwa Khristu. Tikuyenera kukhala ndi chikhalidwe chopembera ndi mpingo umodzi nthawi zonse. Acts 2:42; Hebrews 10:24–25. We gather to worship to help one another grow to maturity in Christ. We must make worship with our church a habit. Preacher: Dr. Joshua Hutchens Cla...
Werenga Baibulo | Read the Bible 16.05.2020 30:19
Machitidwe 2:42; 2 Timoteyo 3:16–17. Kudzera mukuwerenga Baibulo, timamva Mulungu akuyakhula nafe. Khalani ndi dogosolo lakawerenge ka Baibulo komanso yambani kuwerenga. Konzekerani Kuwerenga Baibulo: https://chiphunzitsochoona.com/wp-content/uploads/2020/05/Bible-Reading-Plan-Chichewa.pdf Acts 2:42; 2 Timothy 3:16-17. By reading the Bible, we hear God speak to us. Have a plan for reading the Bibl...
Yambani Kupemphera | Start Praying 11.05.2020 43:34
Kudzera mupemphero, timamva umwana wathu mubanja la Mulungu. Yesu anatiphuzitsa momwe tikuyenerera kupemphera munjira yomwe ikuyenerera ku pereka ulemerero kwa Mulungu. Through prayer, we experience our adoption into God's family. Jesus taught us how to pray in a way that glorifies God. Preacher: Dr. Joshua Hutchens Class: Kukhala Wophunzira: Kukhala Moyo Wosinthika ndi Uthenga Wabwino | Disciples...
Similar podcasts
Replaio is not a podcast publisher; show names, artwork and audio belong to their authors and are distributed through public RSS feeds.