Gospel Life
Chiphunzitso Choona | Sound Doctrine
Sermons and teaching in Chichewa and English
Author
Gospel Life
Category
Podcast website
Latest episode
Apr 24, 2026
Where to listen?
Podcasts in the app Replaio Radio Coming soonPodcasts are coming to the app soon. Install now and be the first to see a whole new take on podcasts
Episodes
Anapereka mzimu wake/He gave up his spirit 03.04.2023 48:09
Yohane 19:30, pamene Yesu anali pamtanda kusausitsa kuti apume, anayangána kumwamba kwa atate ake nati "kwatha." Chinthu china chodabwitsa chinachitika patatha izi. Pamene ife anthu tikamwalira mizimu yathu imatengedwa kwa ife. Koma Yesu anapereka mzimu wake yekha. Imfa yake imapangitsa kuthekera kati ife tikhale opanda mantha ingakhale mavuto abwera. John 19:30, when Jesus was at the cr...
Mulungu ndi wamkulu kuposa mitima yathu/God is greater than our hearts 27.02.2023 40:07
1 Yohane 3:19-24, kulimbika mtima pamaso pa mulungu kumathandiza ife kuzindikira kuti tili pa choonadi ndipo timakhala okhazikika mtima pa maso pa mulungu. Ife timalandira chilichonse tipempha kwa iye, chifukwa timamvera malamulo ake ndi kuchita zimene zimamukondweretsa. Nthawi imene tichita izi; iye amakhala mwa ife ndipo ife timakhala mwa iye. 1 John 3:19-24, as we are strong hearted and stead f...
Chikondi pa wina ndi mnzake ndi m'choonadi/Love for one another and in truth 21.02.2023 1:08:34
1 Yohane 3:11-18, mawu awa akutikumbutsa za chikondi chathu pa wina ndi mnzake makamaka pamene ife tsono ndi ake a mulungu, chikondi chathu chisakhale cha pakamwa koma cha ntchito zathu ndi m'choonadi kuwonetsera chiyanjano chathu ndi mulungu wathu mwa ambuye wathu Yesu Khristu. 1 John 3:11-18, these words are reminding us of our love for one another especially now that we are children of God, our...
Ana A Mulungu/The Children Of God 15.02.2023 47:02
1 Yohane 2:28-3:1-10, mawu a mulungu awa akuthandiza onse omwe ndi ake mulungu kuzindikira kuti pamene ife tagulidwa ndi mwazi wake wa Yesu khristu ndife tsopano ana a mulungu. Ana a mulungu amachita chilungamo ndipo ndiwolungama. Onse omwe alimwa khristu amafanana naye iye. Koma ngati pakati pathu pali ena omwe sachita chilungamo ngakhalenso sakonda m'bale wawo, amenewo siake a mulungu koma a mdi...
Khalani mwa Khristu/Remain in Christ 10.02.2023 38:33
1 Yohane 2:18-27, nthawi zambiri anthu amafunsa kuti kodi 'tili nthawi ya masiku omaliza?' Yankho ndi eya. Nthawi ya masiku omaliza ndi pakati pa kubwera kwa Yesu Khristu koyamba ndi kubwera kwa Yesu Khristu kachiwiri. Bukuli likubweretsa poyera nkhani imene ndiyovuta kuyimvetsa. Kodi okana Khristu abwera liti? Paulo akunena motere pakhaniyi, okana Khristu wamkulu adzabwera koma chidwichathu chikh...
Kondani Mulungu/Love God 07.02.2023 56:35
1 Yohane 2:12-17,chifukwa chachikondi chimene tilinacho pa mulungu wathu, timamumvera ndi kutsatira malamulo ake. Choncho timawonetsera ku dziko lonse kuti ndife ake kudzera muchikondi chomwe tilinacho pa mulungu wathu. Ndichifukwa chake abale tiyeni tipitirize monga okhulupirira komanso okonda mulungu ndi kukana dziko lapansi. 1 John 2:12-17, because of the love we have for God, we continue to lo...
Kumvera Mulungu ndi Malamulo ake/Obedient to God and his commandment 25.01.2023 58:09
1 Yohane 2:3-11, Buku la 1 Yohane likupitiriza kubwera poyera njira zomwe khristu opulumutsidwa akuyenera kupitiriza kuyenda pa nthawi imene khristu wapulumutsidwa. Kumvera mulungu ndi malamulo ake ndi chiwonetsero chachikulu ndi chilungamo chathu kwa anthu kuti ife timankonda mulungu, timakhulupirira mulungu wathu, zonse zimene mulungu atilamulira kuti tichite ife timamvera ndikuchita. 1 John 2:3...
Kuyenda mu kuwunika(khalidwe loyamba)/Walking in the light(the first attribute) 22.01.2023 58:44
1 Yohane 1:5-2:2, kutchulidwa kuti nkhristu sikungapangise munthu kukhala ndi zimene nkhristu ali nazo. Bukuli muli njira zomwe akhristu akuyenera kuyenda pa chikhristu chawo. Chiyambi cha bukuli tikupeza chiphunzitso cha moyo. Akhristu amene alandira moyo ndipo ali ndi moyo tsopano akuyenera kuyenda mu kuwunika chifukwa ali pa chiyanjano ndi mulungu amene ndi kuwunika. 1 John 1:5-2:2, to be calle...
Makhalidwe a chiyanjano mu mpingo/attributes of fellowship in the church 18.01.2023 1:00:10
1 Yohane 1:1-4, moyo weniweni umachokera kwa mulungu ndipo ndi moyo wosatha. Kodi ife tili ndi moyo wosatha? Mulungu amapereka moyo wosatha, ndiye Yesu Khristu. Uthenga wabwino umabweretsa chiyanjano pakati pa akhristu mu mpingo. Ngati tili ndi moyo wosatha, tidzakhala pa chiyanjano ndi atate ndi mwana ndi mzimu woyera ndi wina ndi zake. Tikuyenera kukhala ndi chiyanjano chimene ndi moyo wos...
Za mkati mwa buku la 1 Yohane/Inside the book of 1 John 06.01.2023 1:04:38
1 Yohane, buku limeneli likupezeka ndi uthenga opasa moyo. Nkhani zomwe zikupezeka mu bukuli kwambiri ndi ndondomeko za kayendedwe ka khristu kuti ndi ziti zomwe akuyenera kuchita khristu komanso ndi ziti zomwe sakuyenera kuchita pamene iye wa pulumutsidwa kapena pamene iye watchulidwa kuti ndi khristu. Khristu aliyense amakhala khristu pamene wabatizidwa ndipo pamene mzimu woyera ali mwa iye. Ndo...
Mtima ngati wa Khristu Yesu/A heart like that of Christ Jesus 27.12.2022 57:06
Aphilipi 2:5-8, ma vesi amenewa akulimbikitsa akhristu onse kukhala odzichepetsa monga Yesu Khristu anali odzichepetsa. Yesu anavomera kusiya ulemerero wake ku dziko la kumwamba ndi kubadwira ku banja losauka, kubadwira anthu osauka ndi cholinga choti apeleke chipulumutso ku dziko lonse lapansi ndi kupulumutsa anthu onse ochimwa. Chifukwa cha kudzichepetsa kwa Khristu Yesu lero anthu tonse tili nd...
Chisangalaro choonadi pa kubadwa kwa Yesu Khristu/The real happiness upon the birth of Jesus Christ 20.12.2022 53:26
Mateyu 2:1-15, kubadwa kwa ambuye Yesu m'mitima mwathu ndi chinthu chonyaditsa kwambiri. Ndipo chisangalaro chake ndichamtengo wapatali. Anzeru akum'mawa anakondwera kwambiri poona mfumu yobadwayo. Kodi nankha ife lero tikamulandira Yesu Khristu ndikukhala ambuye ndi mpulumutsi wathu timakondwerera motani? Matthew 2:1-15, The birth of our lord Jesus in our hearts its a priceless gift. And the happ...
Yesu Khristu ndi uthenga wabwino/Jesus Christ is the good news 17.12.2022 48:31
Luka 2:1-14, kubadwa kwa yesu Khristu kunabweretsa chimwemwe pakati pa anthu makamaka okhawo omwe anamudwiwa iye. Ndipo chimwemwe chotere chimapitirira kupezeka pakati pathu. Makamaka mwa ife tonse okhulupirira ndi opulumutsidwa chifukwa timadziwa bwino lomwe kuti Yesu Khristu ndi chifukwa chokhacho tili ndi moyo komanso ndi chiyembekezo. Luke 2:1-14, the birth of Jesus Christ brought happiness am...
Kuyenda m'chikondi/Walking in the love 28.11.2022 1:07:00
Aefeso 4:1-6, Paulo mtumwi akulimbikitsa a khristu kukhala ndi makhalidwe oyenera mayitanidwe awo. Akhale odzichepetsa kwathunthu ndi ofatsa, oleza mtima, ololerana wina ndi mzake. Akhristuwa achite zonsezi moyetsetsa kusunga umodzi wa mzimu umene umatimangilira pamodzi ndi mtendere. Ephesians 4:1-6, the apostle Paul is appealing to the christians to walk worthily of the calling with which t...
Mpingo ndi thupi la Khristu Yesu/A church is the body of Christ Jesus 23.11.2022 1:11:59
Afilipi 2:1-4, mundime yamalemba imeneyi Paulo akuthokoza, akulangiza, akulimbikitsa ndi kudzuzura mpingo omwe iye anawuyambitsa ponena kuti "monga mpingo ndi thupi la Khristu Yesu, ziwalo zake kukhala akhristu sakuyenera kukhala ndi migawano, popeza sitingathe kugawa thupi la Khristu Yesu." Motero akulimbikitsa akhristu kukhala ozichepetsa mu mpingo. Philippians 2:1-4, in this passage Paul is ext...
Milodzo yolodzera chipulumutso/Signs leading to salvation 21.11.2022 51:33
Genesis 11:10-32, mibado yonse kuyambira pa Adamu, Seti, Nowa, Semu komanso abramu yemwe anasinthidwa kukhala Abrahamu ikutitengera kwa Yesu Khristu yemwe ndi chipulumutso cha anthu onse. Ife tonse ndiodala kamba koti tilimunthawi yomwe milodzo inafika kumathero ndipo chipulumutso chinapelekedwa. Ife tingoyenera kukhulupirira Yesu kukhala mpulumutsi ndi ambuye ndipo tipulumutsidwa. Genesis 1...
Kodi umodzi ndi mphamvu?Is oneness a sign of power? 09.11.2022 1:12:31
Genesis 11:1-9, nthawi zambiri timakamba zokhuza umodzi mokondwera mkumati umodzi ndi mphamvu. Kodi ndi chonchodi? Eya, mokuti Baibulo limalimbikitsa umodzi kufikira pakuti Yesu anati, pali awiri nanenso ndimakhala pomwepo. Koma umodzi omwe ulinga wa Nimurodi, ziwani kuti mulungu amadana nawo ndipo amatsika kuzadzetsa kusamvana pakati pa onse ozondosa zabwino kusandusa zoipa. Genesis 11:1-9, most...
Mulungu amakwaniritsa malonjezano ake/God fulfils his promises 01.11.2022 41:18
Genesis 10:1-32, mu chaputara chimenechi tikuona ndandanda wa ana a Nowa. Koma nkhani yayikulu yagona pa Semu. Kuchokera kwa Semu kunabadwa mwana yemwe anabereka mwana yemwe anaberekanso mwana yemwe anali tate wa Abrahamu komwe mbewu ya mzimayi ikudzera kufikira pa Yesu Khristu. Mulungu atalonjeza kwa mzimayi uja mumachaputara oyambirira aja za mbewu yomwe izaphwanya mutu wanjoka mubukuli, tikuona...
Kugonjetsa Zoipa Pakuchita Zabwino/Defeating Evil by Doing Good 27.10.2022 1:02:12
Genesis 9:18-28, Nowa atatuluka mchombo anayamba kulima nthaka monga momwe Adamu ankachitira. Nowa anali munthu woyambilira kulima mphesa. Munkhaniyonse tikuona kuti kumapeto kwake kwa kulima mphesaku kukubweretsa mavuto omwe anatsatiridwa ndi themberero. Tikuonanso kuti ana aamuna a Nowa ndikomwe kunachokera mitundu yonse ya anthu pa dziko lapansi. Zimene nkhaniyi ikutanthauza ndi izi: nthawi zon...
Pangano La Mulungu Ndi Nowa/The Covenant Of God With Noah 20.10.2022 44:22
Genesis 9:8-17, Mulungu atakondweretsedwa ndi Nowa chifukwa cha kumvera kwake, anamudalitsa namuuza kuti "abelekane ndipo adzadze dziko lapansi ndikuligonjetsa." kenaka Mulungu anachita naye pangano Nowa namuuza kuti sazawononganso dziko lapansi ndi madzi. Izi zinali zosangalasa kwa Nowa ndi banja lake. Komatu izi sizikutanthauza kuti Mulungu sazalanganso dziko lapansi chifukwa cha machimo a anthu...
Noah received a blessing through obedience to God/Nowa analandira M'dalitso kudzera mukumvera Mulungu 11.10.2022 56:31
Genesis 9:1-7, Noah did everything that God asked of him, he never questioned God or refuse his commandments. But followed God's instructions through out his entire life even when building the Ark, he kept on following God's own directions. And because of this, God was impressed with Noah, so he blessed him and told him that "be fruitful and multiply, fill the earth and subdue it." This is like wi...
Spiritual Warfare/Nkhondo ya uzimu 06.10.2022 1:12:58
Revelation chapter 8, Dr Eric continues exploring the book of revelation. The book of revelation, for proper understanding of the book, two things to consider; 1) the use of metaphoric language. this is important to take note of, because it would be very difficult to take everything you hear in the book to be literal. for example, when the book talks about the beast of ten horns and the face of a...
Kodi muli mbali iti m'masiku omalizawa?/What side are you on in these ladder days? 21.09.2022 30:25
Chivumbulutso chaputara 7, mu chaputara chimenechi Dr. Eric akupitiliza kubweletsa poyera za nsautso waukulu m'masiku omaliza. Kamvetsetsedwe ka nthawiyi kakupitilirabe kukhala kovutirapo kwa anthu ena kamba kuti kalembedwe kozembayisa kakupitilirabe kupezeka ingakhale mu chaputarachi. Panthawi yomweyo tikuona kuti Paulo akulemba chaputarachi mundondomeko yomwe ingafananizilidwe ndi mapiri omwe pa...
Kupembedza Koona ndi Kuvomereza ndi Mathokozo Chipulumutso cha Mulungu pa anthu ake/A proper worship is a proper response to God's salvation. 19.09.2022 58:51
Genesis 8:15-22, Nowa akutiwonesera mtima omvera. Nowa anadikira mçhombo ngakhale anali akudziwa kuti madzi adali atawuma ndipo akadatha kutuluka, koma iye anadikira lamuro lochokera kwa Mulungu lomuuza kuti atha kutuluka limodzi ndi ziyama zonse zinali ndi iye mçhombomo. Panthawi yomweyo tikuona kuti chinthu chomwe chikukambidwa mobwereza chokhuza kumvera kwa Nowa ndichakuti iye anachita zonse zo...
Chivumbulutso cha nthawi ya "msautso" m'masiku omaliza/The Revelation of the "great tribulation" in the ladder days 15.09.2022 50:22
Chivumbulutso 6:1-6, Abusa a Eric, akubweletsa poyera za msautso omwe ukuza pa dziko la pansi m'masiku omaliza. M'buku la chivumbulutso chaputara chachisanu ndi chimodzi, chikukamba za zimatiro zisanu ndi ziwiri zomwe kumvetsetsa kwake kumakhala kovutilapo chifukwa cha kagwilitsidwe ntchito ka mawu omwe ndi ozembayisa. Chifukwa chake anthu ambiri amakhala ndi mfundo zosiyanasiyana pa khani imeneyi...
Similar podcasts
Replaio is not a podcast publisher; show names, artwork and audio belong to their authors and are distributed through public RSS feeds.