Gospel Life
Chiphunzitso Choona | Sound Doctrine
Sermons and teaching in Chichewa and English
Author
Gospel Life
Category
Podcast website
Latest episode
Apr 24, 2026
Where to listen?
Podcasts in the app Replaio Radio Coming soonPodcasts are coming to the app soon. Install now and be the first to see a whole new take on podcasts
Episodes
Mphamvu za Mulungu Zosunga Oyera Mtima 07.05.2020 49:37
Chifukwa cha mphamvu za Mulungu ndi chifuniro chake, anthu woyera mtima apirira mu chikulupirira chawo mpaka kumapeto kwa moyo. Preacher: Isaac Dzimbiri Class: Kudzama Choonadi Series: Kupirira kwa Oyera Mtima Chikhulupiriro Chawo
Batizidwani | Be Baptized 05.05.2020 26:30
Ubatizo ndi njira yoyambirira ya kumvera monga mKhristu watsopano. Uma onetsera kwa aliyense yemwe alikunja zomwe Mulungu wachita kuti mwa munthu. Baptism is your first step of obedience as a new Christian. It is the public sign of your faith. It shows to everyone outside what God has done inside. Preacher: Dr. Joshua Hutchens Class: Kukhala Wophunzira: Kukhala Moyo Wosinthika ndi Uthenga Wabwino...
Uthenga Wabwino ndi Mphamvu ya Mulungu | The Gospel is the Power of God 03.05.2020 31:46
Aroma 1:16–17. Uthenga Wabwino ndi mphamvu ya Mulungu yopulumutsa chifukwa mu Uthenga Wabwino mphatso ya Mulungu ya chilungamo ya onetsedwa. Romans 1:16–17. The gospel is the power of God for salvation because in the gospel God's gift of righteousness is revealed. Preacher: Dr. Joshua Hutchens Class: Kuyenda m'Choonadi | Walking in Truth Series: Aroma | Romans Translator: Isaac Dzimbiri
Kodi ndi chifukwa chiyani ukuyenera kudziwa kuti ndiwe wochimwa usanapulumutsidwe? 02.05.2020 19:16
Funsa Mafunso: Kodi ndi chifukwa chiyani ukuyenera kudziwa kuti ndiwe wochimwa usanapulumutsidwe? Ask a Question: Why must you know you are a sinner before you can be saved? Preacher: Dr. Joshua Hutchens Translator: Isaac Dzimbiri
Chikondi cha Mulungu Chitsimikiza Kupirira kwa Oyera Mtima m'Chikhulupiriro 30.04.2020 41:04
2 Timoteyo 1:9. Kupirira kwa anthu wokhulupirira kwa khazikika mu chikondi chosatha cha Mulungu, yemwe anatipatiratu chisomo chake mwa Yesu Khristu kutiwombola ife ku machimo athu. Preacher: Isaac Dzimbiri Class: Kudzama Choonadi Series: Kupirira kwa Oyera Mtima Chikhulupiriro Chawo
Timagwira ntchito chifukwa Mulungu akugwira ntchito | We work because God works 28.04.2020 26:14
Mulungu wakulenga iwe kukhala watsopano. Tsono timamvera Mulungu chifukwa timamukonda Mulunguyo, ndipo timamumvera, Mulungu amagwira ntchito mwaife. God has made you new. So we obey God because we love God, and as we obey, God works in us. Preacher: Dr. Joshua Hutchens Class: Kukhala Wophunzira: Kukhala Moyo Wosinthika ndi Uthenga Wabwino | Discipleship: Living the Gospel Translator: Isaac Dzimbir...
Mulungu wagonjetsa kudzera mwa Mwana wake | God has conquered through his Son 26.04.2020 31:01
Aroma 1:8–15. Chigonjetso cha Mwana wa Mulungu chitha kuonekera mu chikhulupiriro chathu komanso mukulalikira Uthenga Wabwino ku mayiko onse. Romans 1:8–15. The victory of God's Son can be seen in our faith and in the preaching of the gospel to every nation. Preacher: Dr. Joshua Hutchens Class: Kuyenda m'Choonadi | Walking in Truth Series: Aroma | Romans Translator: Isaac Dzimbiri Episode Page: ht...
Dongosola la Mulungu pa Chipulumutso cha Oyera Mtima 23.04.2020 29:39
Aefeso 1:4–7; Aroma 8:29–30. Chipulumutso ya oyera mtima china yamba ndi Mulungu, ndipo chidzamulizidwa ndi Mulungu. Chifukwa choti Mulungu amatsiriza ndogosolo lomwe wa liyamba adzatsirizanso dogosolo la chipulumutso cha oyera mtima. Preacher: Isaac Dzimbiri Class: Kudzama Choonadi Series: Kupirira kwa Oyera Mtima Chikhulupiriro Chawo Episode Page: https://chiphunzitsochoona.com/sermon/dongosola-...
Mwapatulidwa ku Uthenga Wabwino | You are set apart for the gospel 22.04.2020 36:39
Aroma 1:1–7. Mulungu adatipatulidwa ife kuti tikalalikire Uthenga Wabwino ku mitundu yonse kwa ulemerero wa dzina la Mulungu. Romans 1:1–7. God set us apart to preach the gospel of Jesus Christ to all nations for the glory of God’s name. Preacher: Dr. Joshua Hutchens Class: Kuyenda m'Choonadi | Walking in Truth Series: Aroma | Romans Translator: Isaac Dzimbiri Episode Page: https://chiphunzitsocho...
Vomereza ndi Kukhulupirira | Confess and Believe 19.04.2020 21:14
Part 4 of 4 in Mphamvu za Mulungu Zopulumutsa | The Power of God for Salvation
Yesu ndi Mpulumutsi wanu | Jesus is your Savior 12.04.2020 15:06
Part 3 of 4 in Mphamvu za Mulungu Zopulumutsa | The Power of God for Salvation
Iwe ndiwe wochimwa | You are a sinner 29.03.2020 20:11
Part 2 of 4 in Mphamvu za Mulungu Zopulumutsa | The Power of God for Salvation
Mulungu ndi wabwino | God is good 22.03.2020 15:28
Part 1 of 4 in Mphamvu za Mulungu Zopulumutsa | The Power of God for Salvation
Similar podcasts
Replaio is not a podcast publisher; show names, artwork and audio belong to their authors and are distributed through public RSS feeds.