Gospel Life

Chiphunzitso Choona | Sound Doctrine

Sermons and teaching in Chichewa and English

Koniecznie odwiedź stronę podcastu i wesprzyj twórcę: chiphunzitsochoona.com

Autor

Gospel Life

Kategoria

Religion

Strona podcastu

chiphunzitsochoona.com

Ostatni odcinek

24 kwi 2026

Gdzie słuchać?

Podcasty w aplikacji Replaio Radio Już wkrótce

Podcasty trafią do aplikacji już wkrótce. Zainstaluj teraz i jako pierwszy zobacz nowe podejście do podcastów

Pobierz z Google Play Zainstaluj za darmo Android prawie 10 mln pobrań · ocena 4,8 iOS niedługo

Odcinki

Mphamvu za Mulungu Zosunga Oyera Mtima 07.05.2020

Chifukwa cha mphamvu za Mulungu ndi chifuniro chake, anthu woyera mtima apirira mu chikulupirira chawo mpaka kumapeto kwa moyo. Preacher: Isaac Dzimbiri Class: Kudzama Choonadi Series: Kupirira kwa Oyera Mtima Chikhulupiriro Chawo

Batizidwani | Be Baptized 05.05.2020

Ubatizo ndi njira yoyambirira ya kumvera monga mKhristu watsopano. Uma onetsera kwa aliyense yemwe alikunja zomwe Mulungu wachita kuti mwa munthu. Baptism is your first step of obedience as a new Christian. It is the public sign of your faith. It shows to everyone outside what God has done inside. Preacher: Dr. Joshua Hutchens Class: Kukhala Wophunzira: Kukhala Moyo Wosinthika ndi Uthenga Wabwino...

Uthenga Wabwino ndi Mphamvu ya Mulungu | The Gospel is the Power of God 03.05.2020

Aroma 1:16–17. Uthenga Wabwino ndi mphamvu ya Mulungu yopulumutsa chifukwa mu Uthenga Wabwino mphatso ya Mulungu ya chilungamo ya onetsedwa. Romans 1:16–17. The gospel is the power of God for salvation because in the gospel God's gift of righteousness is revealed. Preacher: Dr. Joshua Hutchens Class: Kuyenda m'Choonadi | Walking in Truth Series: Aroma | Romans Translator: Isaac Dzimbiri

Kodi ndi chifukwa chiyani ukuyenera kudziwa kuti ndiwe wochimwa usanapulumutsidwe? 02.05.2020

Funsa Mafunso: Kodi ndi chifukwa chiyani ukuyenera kudziwa kuti ndiwe wochimwa usanapulumutsidwe? Ask a Question: Why must you know you are a sinner before you can be saved? Preacher: Dr. Joshua Hutchens Translator: Isaac Dzimbiri

Chikondi cha Mulungu Chitsimikiza Kupirira kwa Oyera Mtima m'Chikhulupiriro 30.04.2020

2 Timoteyo 1:9. Kupirira kwa anthu wokhulupirira kwa khazikika mu chikondi chosatha cha Mulungu, yemwe anatipatiratu chisomo chake mwa Yesu Khristu kutiwombola ife ku machimo athu. Preacher: Isaac Dzimbiri Class: Kudzama Choonadi Series: Kupirira kwa Oyera Mtima Chikhulupiriro Chawo

Timagwira ntchito chifukwa Mulungu akugwira ntchito | We work because God works 28.04.2020

Mulungu wakulenga iwe kukhala watsopano. Tsono timamvera Mulungu chifukwa timamukonda Mulunguyo, ndipo timamumvera, Mulungu amagwira ntchito mwaife. God has made you new. So we obey God because we love God, and as we obey, God works in us. Preacher: Dr. Joshua Hutchens Class: Kukhala Wophunzira: Kukhala Moyo Wosinthika ndi Uthenga Wabwino | Discipleship: Living the Gospel Translator: Isaac Dzimbir...

Mulungu wagonjetsa kudzera mwa Mwana wake | God has conquered through his Son 26.04.2020

Aroma 1:8–15. Chigonjetso cha Mwana wa Mulungu chitha kuonekera mu chikhulupiriro chathu komanso mukulalikira Uthenga Wabwino ku mayiko onse. Romans 1:8–15. The victory of God's Son can be seen in our faith and in the preaching of the gospel to every nation. Preacher: Dr. Joshua Hutchens Class: Kuyenda m'Choonadi | Walking in Truth Series: Aroma | Romans Translator: Isaac Dzimbiri Episode Page: ht...

Dongosola la Mulungu pa Chipulumutso cha Oyera Mtima 23.04.2020

Aefeso 1:4–7; Aroma 8:29–30. Chipulumutso ya oyera mtima china yamba ndi Mulungu, ndipo chidzamulizidwa ndi Mulungu. Chifukwa choti Mulungu amatsiriza ndogosolo lomwe wa liyamba adzatsirizanso dogosolo la chipulumutso cha oyera mtima. Preacher: Isaac Dzimbiri Class: Kudzama Choonadi Series: Kupirira kwa Oyera Mtima Chikhulupiriro Chawo Episode Page: https://chiphunzitsochoona.com/sermon/dongosola-...

Mwapatulidwa ku Uthenga Wabwino | You are set apart for the gospel 22.04.2020

Aroma 1:1–7. Mulungu adatipatulidwa ife kuti tikalalikire Uthenga Wabwino ku mitundu yonse kwa ulemerero wa dzina la Mulungu. Romans 1:1–7. God set us apart to preach the gospel of Jesus Christ to all nations for the glory of God’s name. Preacher: Dr. Joshua Hutchens Class: Kuyenda m'Choonadi | Walking in Truth Series: Aroma | Romans Translator: Isaac Dzimbiri Episode Page: https://chiphunzitsocho...

Vomereza ndi Kukhulupirira | Confess and Believe 19.04.2020

Part 4 of 4 in Mphamvu za Mulungu Zopulumutsa | The Power of God for Salvation

Yesu ndi Mpulumutsi wanu | Jesus is your Savior 12.04.2020

Part 3 of 4 in Mphamvu za Mulungu Zopulumutsa | The Power of God for Salvation

Iwe ndiwe wochimwa | You are a sinner 29.03.2020

Part 2 of 4 in Mphamvu za Mulungu Zopulumutsa | The Power of God for Salvation

Mulungu ndi wabwino | God is good 22.03.2020

Part 1 of 4 in Mphamvu za Mulungu Zopulumutsa | The Power of God for Salvation

Słuchaj podcastu Chiphunzitso Choona | Sound Doctrine w Replaio

Radio i podcasty w jednej aplikacji - za darmo, bez zakładania konta. Zainstaluj już dziś i nie przegap premiery

Pobierz z Google Play

Replaio nie jest wydawcą podcastów; nazwy audycji, okładki i audio należą do ich autorów i są rozpowszechniane przez publiczne kanały RSS