Thru the Bible Chichewa

TTB Chichewa

Pologalamu ya Tisanthule Baibulo ndi gawo limodzi lautumiki, ophunzitsa Baibulo, otchedwa ulendo m??baibulo (Thru the Bible). Mndandanda wamapogalamuwu unakonzedwa ndi Dr. J. Vernon McGee ndipo unatanthauzidwa mu zilankhulo zoposa zana zimodzi (100). Zinakonzedwa kuti pologalamu imodzi idzikhala ya mphindi makumi atatu (30) ndipo kuti pomaliza zidzathe kuthandiza omvera kumvetsetsa Baibulo lonse. Ndipo pakali pano mapologalamu onsewa tawaika pamakina a Intaneti. Ndife oyamika kuti mwasankha kuphunzira zambiri zokhudza mau a Mulungu kudzera mmapologalamuwa. Tikukulimbikitsani kuti mudzimvera po...

Não deixe de visitar o site do podcast e apoiar quem o produz: ttb.twr.org

Autor

Thru the Bible Chichewa

Categoria

Religion

Site do podcast

ttb.twr.org

Último episódio

30 de out de 2024

Onde ouvir?

Podcasts no app Replaio Radio Em breve

Os podcasts estão chegando ao app. Instale agora e seja o primeiro a descobrir um jeito totalmente novo de curtir podcasts

Baixe no Google Play Instale grátis Android 5 mi+ downloads · nota 4,8 iOS em breve

Episódios

Ulamuliro Woipa Wa Manase 30.10.2024
Kuchiritsidwa Kwa Hezekiya, Cholakwa Ndi Imfa Yake 29.10.2024
Nkhawa Ya Hezekiya Ndi Ulosi Wa Yesaya 28.10.2024
Chitsitsimutso Chikudza Ndi Hezekiya Ndipo Mulungu Ayesa Chikhulupiriro Cha A Yuda 25.10.2024
Ahazi Akhala Mfumu Ya Yuda Pamene Israyeli Atengedwa Ukapolo 24.10.2024
Ntchito Zomaliza Za Elisa; Mafumu Abwino Ndi Oipa A Israyeli 23.10.2024
Yoasi Akhala Mfumu Ndi Ulamuliro Wake 22.10.2024
Yehu Akhala Mfumu Ya Israyeli Ndi Chilango Pa Nyumba Ya Ahabu 21.10.2024
Elisa Akwaniritsa Malonjezo Ake Ndi Chilango Kwa Oipa 18.10.2024
Elisa Ayandamitsa Nkhwangwa Pa Madzi Ndi Chiwembu Cha Elisa Ku 17.10.2024
Mbiri Ya Namaani Wa Ku Syria 16.10.2024
Elisa Alowa M’malo Mwa Eliya Ndi 15.10.2024
Moto Wa Kumwamba Woteteza Eliya Kwa Ahaziya Ndipo Eliya Akwera Kumwamba 14.10.2024
Ahabu Ndi Munda Wa Naboti; Ahabu Ndi Mneneri Mikaya 11.10.2024
Eliya Ali Pansi Pa Mtengo Wa Tsanya: Israyeli Amenyana Ndi Syria 10.10.2024
Eliya Adzudzula Ahabu Ndipo Yehova Atsutsana Ndi Baala Pa Phiri La Kalimeri 09.10.2024
Ukwati Wa Yezeberi Ndi Ahabu Ndi Kuti Eliya Alengeza Za Chilala Kwa Zaka Zitatu 08.10.2024
Imfa Ya Rehabiamu Ndi Yerobiamu; Mafumu A Ufumu Wogawika 07.10.2024
Chilango Pa Yerobiamu Ndi Yuda 04.10.2024
Zinthu Zochititsa Manyazi Ndi Imfa Ya Solomoni; Kugawika Kwa Ufumu Pakati Pa Rehabiamu Ndi Yerobiamu 03.10.2024
Ntchito Yomanga Kachisi Ndi Mwambo Wopereka Kachisi 02.10.2024
Ntchito Yomanga Kachisi Ndi 01.10.2024
Kukonzekera Ndi Kumanga Kachisi Wa Mulungu 30.09.2024
Chopempha Cha Solomoni; Pemphero Lake Liyankhidwa Ndi Ukulu Wa Ufumu Wake 27.09.2024
Upangiri Wa Davide Kwa Solomoni Ndipo Solomoni Apempha Nzeru 26.09.2024

Ouça o podcast TTB Chichewa no Replaio

Rádio e podcasts em um só app - grátis e sem cadastro. Instale hoje e não perca o lançamento

Baixe no Google Play

O Replaio não é o publicador dos podcasts; os nomes dos programas, as capas e o áudio pertencem aos seus autores e são distribuídos por feeds RSS públicos