Thru the Bible Chichewa

TTB Chichewa

Religion EN ↓ 261 episodes

Pologalamu ya Tisanthule Baibulo ndi gawo limodzi lautumiki, ophunzitsa Baibulo, otchedwa ulendo m??baibulo (Thru the Bible). Mndandanda wamapogalamuwu unakonzedwa ndi Dr. J. Vernon McGee ndipo unatanthauzidwa mu zilankhulo zoposa zana zimodzi (100). Zinakonzedwa kuti pologalamu imodzi idzikhala ya mphindi makumi atatu (30) ndipo kuti pomaliza zidzathe kuthandiza omvera kumvetsetsa Baibulo lonse. Ndipo pakali pano mapologalamu onsewa tawaika pamakina a Intaneti. Ndife oyamika kuti mwasankha kuphunzira zambiri zokhudza mau a Mulungu kudzera mmapologalamuwa. Tikukulimbikitsani kuti mudzimvera po...

Be sure to visit the podcast's website and support the creator: ttb.twr.org

Author

Thru the Bible Chichewa

Category

Religion

Podcast website

ttb.twr.org

Latest episode

Oct 30, 2024

Where to listen?

Podcasts in the app Replaio Radio Coming soon

Podcasts are coming to the app soon. Install now and be the first to see a whole new take on podcasts

Get it on Google Play Install for free Android almost 10M downloads · 4.8 rating iOS soon

Episodes

Yesu Akumana Ndi Mkazi Pa Chitsime 28.02.2024
Ulendo Wa Nikodemo Ndi Umboni Wa Yohane M’batizi 27.02.2024
Yesu Agwiritsa Ntchito Mau Poyeretsa Kachisi Ndi Nkhani Ya Nikodemo 26.02.2024
Ntchito Yoyamba Ya Yesu Pa Ukwati Wa Ku Kana 23.02.2024
Umboni Wochitira Yesu Wa Anthu Anayi 22.02.2024
Umunthu Wa Mwana Wa Mulungu 21.02.2024
Mau Auuluridwa /Afotokonzeredwa 20.02.2024
Chilango Cha Amidyani, Rubeni Ndi Gadi Afuna Dziko Lawo, lamulo La Kutenga Dziko, Malire A Dziko Lamalonjezano, Midzi Ya Alevi Ndi Lamulo Lacholowa 19.02.2024
Kupitiliza Kuona Za Lamulo La Kaperekedwe Ka Nsembe, Ndi Malumbiro 16.02.2024
Cholowa Cha Wana Wa Akazi, Mose Akonzekera Kufa, Zopereka Ndi Kulambira Koona 15.02.2024
Ulosi Wachinayi, Nzeru Ya Balamu Ndi Chiwerengero Cha M’badwo Watsopano 14.02.2024
Balaki Afuna Baalamu Kuti Atemberere Israyeli, Koma Baalamu Adalitsa Israyeli 13.02.2024
Chigonjetso Cha A Israyeli, Kudandaula Kwa Chisanu Ndi Chitatu, Njoka Ya Mkuwa, Nyimbo Yachiyamiko Ndi Za Balak Ndi Balaamu 12.02.2024
Kudandaula Pa Kadeshi, Madzi Aturuka 09.02.2024
Aroni Ndi Alevi Akhazikitsidwa Pa Ntchito Yawo, Ndi Kuunika Udindo Wawo 08.02.2024
Kuukira Kwa Kukulu Ndikutsatira Chilango Chachikulu, Komanso Kuukanso Kwa Aroni 07.02.2024
Kuunikanso Kuti Chikonzero Cha Yehova Sichidaonongeke, Chilango Cha Imfa Posasunga Sabata, Kuukira Kwa Kora 06.02.2024
Mose Atuma Akazonde, Israyeli Sakukhulupilira Mulungu, Chilango Cha Mulungu Ndi Kulapa Kwa Israyeli 05.02.2024
Mana, Mose Adandaula, Mulungu 02.02.2024
Malipenga A Siliver, Mpongozi Wa Mose Ndipo A Israyeli Ayamba Kuyenda Ndipo Adandaula 01.02.2024
Kuwala Kuchokera Kuchoyikapo Nyali, Alevi Ayeretsedwa, Paskha Ndi Kutsogoleredwa Kwa Israyeli 31.01.2024
Kufunika Kwa Lumbiro La Unanziri Ndi Madalitso Autatu Wa Mulungu Ndi mphatso zake 30.01.2024
Kudetsedwa Kudzera Mwa Nthenda Ndi Uchimo 29.01.2024
Pfuko La Alevi Pamodzi Ndi Ntchito Yawo, Lipatsidwa Kwa Wansembe Wamkulu 26.01.2024
Mtsitsi Kapena Muzu Wa Ana A Israyeli Ndi Kakhalidwe Kadongosolo Ka Pa Chigono 25.01.2024

Listen to the TTB Chichewa podcast in Replaio

Radio and podcasts in one app - free, with no sign-up. Install today and do not miss the launch

Get it on Google Play

Replaio is not a podcast publisher; show names, artwork and audio belong to their authors and are distributed through public RSS feeds.